Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 9:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anaphunzitsa ophunzira ace, nanena nao, kuti, Mwana wa munthu aperekedwa m'manja a anthu, ndipo adzamupha Iye; ndipo ataphedwa, adzauka pofika masiku atatu.

Werengani mutu wathunthu Marko 9

Onani Marko 9:31 nkhani