Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 9:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Yesu anaona kuti khamu la anthu lirikuthamangira pamodzi, anadzudzula mzimu woipawo, nanena ndi uwo, Mzimu wosalankhula ndi wogontha iwe, Ine ndikulamula iwe, turuka mwa iye, ndipo usalowenso mwa iye.

Werengani mutu wathunthu Marko 9

Onani Marko 9:25 nkhani