Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 6:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamalo ponse sakulandirani, kapena kumvera inu, pakucoka kumeneko, sansani pfumbi liri ku mapazi anu, likhale mboni ya kwa iwo.

Werengani mutu wathunthu Marko 6

Onani Marko 6:11 nkhani