Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 5:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo anafika tsidya lina la nyanja, ku dziko la Agerasa,

2. Ndipo pameneadaturuka mungalawa, pomwepo anakomana naye munthu woturuka kumanda wa mzimu wonyansa,

3. amene anayesa nyumba yace kumanda; ndipo palibe munthu anakhoza kummanganso, inde ngakhale ndi unyolo;

Werengani mutu wathunthu Marko 5