Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 2:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Palibe munthu asokerera cigamba ca nsaru yaiwisi pa copfunda cakale; pena cimene coti cidzakonza cizomolapo, catsopanoco cizomoka pa cakaleco, ndipo ciboo cikulapo.

Werengani mutu wathunthu Marko 2

Onani Marko 2:21 nkhani