Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 2:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo alembi a kwa Afarisi, pakuona kuti alinkudya nao ocimwa ndi amisonkho, ananena ndi ophunzira ace, Uyu akudya ndi kumwa nao amisonkho ndi ocimwa.

Werengani mutu wathunthu Marko 2

Onani Marko 2:16 nkhani