Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 15:45-47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

45. Ndipo pamene anacidziwa ndi kenturiyo, anamninkha Yosefe ntembowo.

46. Ndipo anagula oafuta, namtsitsa Iye, namkulunga n'bafutamo, namuika m'manda osenedwa m'thanthwe; nakunkhunicira mwala pa khomo la manda.

47. Ndipo Maliya wa Magadala ndi Maliya amace wa Yose anapenya pomwe anaikidwapo.

Werengani mutu wathunthu Marko 15