Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 14:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pomwepo, Iye ali cilankhulire, anadza Yudase, mmodzi wa khumi ndi awiriwo, ndipo pamodzi naye khamu la anthu, ali nao malupanga ndi mikunkhu, ocokera kwa ansembe akuru ndi alembi ndi akuru.

Werengani mutu wathunthu Marko 14

Onani Marko 14:43 nkhani