Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 14:17-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Ndipo pofika madzulo anadza Iye pamodzi ndi khumi ndi awiriwo.

18. Ndipo pamene anaseama iwo kudya, Yesu anati, Ndithu ndinena ndi inu, Mmodzi wa inu adzandipereka Ine, ndiye wakudya ndi Ine pamodzi.

19. Anayamba iwo kukhala ndi cisoni, ndi kunena naye mmodzi mmodzi, kuti, Ndine kodi?

Werengani mutu wathunthu Marko 14