Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 12:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anafika, ananena naye, Mphunzitsi, tidziwa kuti muli woona, ndipo simusamala munthu; pakuti simuyang'ana nkhope ya anthu, koma muphunzitsa njira ya Mulungu moona: Nkuloleka kodi kupereka msonkho kwa Kaisara, kapena iai?

Werengani mutu wathunthu Marko 12

Onani Marko 12:14 nkhani