Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 10:51-52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

51. Ndipo Yesu anamyankha, nati, Ufuna kuti ndikucitire ciani? Ndipo wakhunguyo anati kwa Iye, Raboni, ndilandire kuona kwanga.

52. Ndipo Yesu anati kwa iye, Muka; cikhulupiriro cako cakupulumutsa iwe. Ndipo pomwepo anapenyanso; namtsata Iye panjira.

Werengani mutu wathunthu Marko 10