Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 10:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anali m'njira alinkukwera kunka ku Yerusalemu; ndipo Yesu analikuwatsogolera; ndipo iwo anazizwa; ndipo akumtsatawo anacita mantha. Ndipo Iye anatenganso khumi ndi awiriwo, nayamba kuwauza zinthu zimene zidzamfikira Iye,

Werengani mutu wathunthu Marko 10

Onani Marko 10:32 nkhani