Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 7:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10 Uyu ndiye amene anali mu Mpingo m'cipululu pamodzi ndi mngelo wakulankhula naye m'phiri la Sina, ndi makolo athu: amene analandira maneno amoyo akutipatsa ife;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7

Onani Macitidwe 7:38 nkhani