Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anauka ena a iwo ocokera m'sunagoge wa Alibertino, ndi Akurenayo, ndi Aalesandreyo, ndi mwa iwo a ku Kilikiya ndi ku Asiya, natsutsana ndi Stefano.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 6

Onani Macitidwe 6:9 nkhani