Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 6:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mau amene anakonda unyinji wonse; ndipo anasankha Stefano, ndiye munthu wodzala ndi cikhulupiriro ndi Mzimu Woyera, ndi Filipo, ndi Prokoro, ndi Nikanora ndi Timo, ndi Parmena, ndi Nikolao, ndiye wopinduka wa ku Antiokeya:

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 6

Onani Macitidwe 6:5 nkhani