Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 6:13-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. naimika mboni zonama, zakunena, Munthu ameneyo saleka kunenera malo oyera amene, ndi cilamulo;

14. pakuu tinamumva iye alikunena, kuti, Yesu Mnazarayo amene adzaononga malo ano, nadzasanduliza miyambo imene Mose anatipatsa.

15. Ndipo anampenyetsetsa onse akukhala m'bwalo la akulu, naona nkhope yace ngati nkhope ya mnaelo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 6