Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

zindikirani inu nonse, ndi anthu onse a Israyeli, kuti m'dzina la Yesu Kristu Mnazarayo, amene inu munampacika pamtanda, amene Mulungu anamuukitsa kwa akufa, mwa Iyeyu munthuyu aimirirapo pamaso panu, wamoyo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 4

Onani Macitidwe 4:10 nkhani