Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 3:25-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Inu ndinu ana a aneneri, ndi a panganolo Mulungu anapangana ndi makolo anu ndi kunena kwa Abrahamu, Ndipo mu mbeu yako mafuko onse a dziko adzadalitsidwa.

26. Kuyambira ndi inu, Mulungu, ataukitsa Mwana wace, anamtuma kukudalitsani inu, ndi kukubwezani yense ku zoipa zace.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 3