Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 28:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene adampangira tsiku, anadza ku nyumba yace anthu ambiri; amenewo anawafotokozera, ndikucitira umboni Ufumu wa Mulungu, ndi kuwakopa za Yesu, zocokera m'cilamulo ca Mose ndi mwa aneneri, kuyambira mamawa kufikira madzulo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 28

Onani Macitidwe 28:23 nkhani