Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 27:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene atakhala nthawi yaikuru osadya kanthu, Paulo anaimirira pakati pao, nati, Amuna inu, mukadamvera ine, osacoka ku Krete, osadzitengera kuonongeka ndi kutayika kumene.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 27

Onani Macitidwe 27:21 nkhani