Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 26:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cimenenso ndinacita m'Yerusalemu: ndipo ndinatsekera ine oyera mtima ambiri m'ndende, popeza ndidalandira ulamuliro wa kwa ansembe akulu; ndiponso pophedwa iwo, ndinabvomerezapo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 26

Onani Macitidwe 26:10 nkhani