Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 25:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Festo anati, Mfumu Agripa, ndi amuna inu nonse muli nafe pano pamodzi, muona uyu, amene unyinji wonse wa Ayuda anandiuza za iye, ku Yerusalemu ndi kunonso, ndi kupfuula kuti sayeneranso kukhala ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 25

Onani Macitidwe 25:24 nkhani