Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 24:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene anamfotokozera za cilungamo, ndi cidziletso, ndi ciweruziro cirinkudza, Felike anagwidwa ndi mantha, nayankha, Pita tsopano; ndipo ndikaona nthawi, ndidzakuitana iwe.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 24

Onani Macitidwe 24:25 nkhani