Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 23:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndipo anamtenga, napita naye kwa kapitao wamkuru, nati, Wam'nsingayo Paulo anandiitana, nandipempha ndidze naye mnyamata uyu kwa inu, ali nako kanthu kakulankhula ndi inu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23

Onani Macitidwe 23:18 nkhani