Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 23:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero tsopano inu ndi bwalo la akuru muzindikiritse kapitao wamkuru kuti atsikenaye kwa inu, monga ngati mufuna kudziwitsitsa bwino za iye; koma tadzikonzeratu timuphe asanayandikire iye.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23

Onani Macitidwe 23:15 nkhani