Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 22:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ine ndine munthu Myuda, wobadwa m'Tariso wa Kilikiya, koma ndaleredwa m'mzinda muno, pa mapazi a Gamaliyeli, wolangizidwa monga mwa citsatidwe ceni ceni ca cilamulo ca makolo athu, ndipo ndinali wacangu, colinga kwa Mulungu, monga muli inu nonse lero;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 22

Onani Macitidwe 22:3 nkhani