Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 21:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

napfuula, Amuna a Israyeli, tithandizeni; ameneyu ndi munthu uja anaphunzitsa onse ponsepo ponenera anthu, ndi cilamulo, ndi malo ano; ndiponso anatenga Ahelene nalowa nao m'Kacisi, nadetsa malo ana oyera.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21

Onani Macitidwe 21:28 nkhani