Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 21:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza kwa ife natenga lamba la Paulo, nadzimanga yekha manja ndi mapazi, nati, Atero Mzimu Woyera, Munthu mwini lamba ili, adzammanga kotero Ayuda a m'Yerusalemu, nadzampereka m'manja a amitundu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21

Onani Macitidwe 21:11 nkhani