Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 20:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu sindiuyesa kanthu moyo, wanga, kuti uli wa mtengo wace kwa ine ndekha; kotero kuti ndikatsirize njira yanga, ndi utumiki ndinaulandira kwa Ambuye Yesu, kucitira umboni Uthenga Wabwino wa cisomo ca Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 20

Onani Macitidwe 20:24 nkhani