Ndipo litaleka phokoso, Paulo anaitana ophunzirawo, ndipo m'mene anawacenjeza, analawirana nao, naturuka kunka ku Makedoniya.