Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 2:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo pakufika tsiku la Penteskoste, anali onse pamodzi pa malo amodzi.

2. Ndipo mwadzidzidzi anamveka mau ocokera Kumwamba ngati mkokomo wa mphepo yolimba, nadzaza nyumba yonse imene analikukhalamo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 2