Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 19:39-41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

39. Koma ngati mufuna kanthu ka zinthu zina, kadzakonzeka m'msonkhano wolamulidwa.

40. Pakutinso palipo potiopsya kuti adzatineneza za cipolowe ca lero; popeza palibe cifukwa ca kufotokozera za cipiringu cimene.

41. Ndipo pamene ananena izi, anamasula msonkhano.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19