Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 19:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturutsa Alesandro m'khamumo, kumturutsa iye Ayuda. Ndipo Alesandro anatambasula dzanja, nafuna kudzikanira kwa anthu adasonkhanawo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19

Onani Macitidwe 19:33 nkhani