Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 18:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacoka kumeneko, nalowa m'nyumba ya munthu, dzina lace Tito Yusto, amene anapembedza Mulungu, nyumba yace inayandikizana ndi sunagoge.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 18

Onani Macitidwe 18:7 nkhani