Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 18:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene iye anafuna kuoloka kunka ku Akaya, abale anamfulumiza, ndi kulembera akalata kwa akuphunzira kuti amlandire: ndipo pamene anafika, iye anathangata ndithu iwo akukhulupira mwa cisomo;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 18

Onani Macitidwe 18:27 nkhani