Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 18:13-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. kuti, Uyu akopa anthu apembedze Mulungu pokana cilamulo.

14. Koma pamene Paulo anati atsegule pakamwa pace, Galiyo anati kwa Ayuda, Ukadakhala mlandu wa cosalungama, kapena dumbo loipa, Ayuda inu, mwenzi nditakumverani inu;

15. koma akakhala mafunso a mau ndi maina ndi cilamulo canu; muyang'ane inu nokha; sindifuna kuweruza zimenezi.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 18