Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 17:7-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

7. amene Yasoni walandira; ndipo onsewo acita zokana malamulo a Kaisara; nanena kuti pali mfumu yina, Yesu.

8. Ndipo anabvuta anthu, ndi akuru a mudzi, pamene anamva zimenezi.

9. Ndipo pamene analandira cikole kwa Yasoni ndi enawo, anawamasula.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17