Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 17:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Ayuda anadukidwa mtima, natenga anthu ena oipa acabe a pabwalo, nasonkhanitsa khamu la anthu, nacititsa phokoso m'mudzi; ndipo anagumukira ku nyumba ya Yasoni, nafuna kuwaturutsira kwa anthu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17

Onani Macitidwe 17:5 nkhani