Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 16:39-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

39. Ndipo anadza nawapembedza; ndipo pamene anawaturutsa, anawapempha kuti acoke pamudzi.

40. Ndipo anaturukam'ndendemo, nalowa m'nyumba ya Lidiya: ndipo pamene anaona abale, anawasangalatsa, namuka.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16