Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 16:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene anautsidwa kutulo mdindoyo, anaona kuti pa makomo a ndende panatseguka, ndipo anasolola lupanga lace, nati adziphe yekha, poyesa kuti am'ndende adathawa.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:27 nkhani