Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 16:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene anabatizidwa iye ndi a pabanja pace anatidandaulira ife, kuti, Ngati mwandiyesera ine wokhulupirika kwa Ambuye, mulowe m'nyumba yanga, mugone m'menemo. Ndipo anatiumiriza ife.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:15 nkhani