Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 16:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku la Sabata tinaturuka kumudzi kunka ku mbali ya mtsinje, kumene tinaganizira kuti amapempherako; ndipo tinakhala pansi ndi kulankhula ndi akazi amene adasonkhana,

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:13 nkhani