Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 16:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anafikanso ku Derbe ndi Lustra; ndipo taonani, panali wophunzira wina pamenepo, dzina lace Timoteo, amace ndiye Myuda wokhulupira; koma atate wace ndiye Mhelene.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:1 nkhani