Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 15:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene panali mafunsano ambiri, Petro anaimirira, nati kwa iwo, Abale, mudziwa kuti poyamba Mulungu anasankha mwa inu, kuti m'kamwa mwanga amitundu amve mau a Uthenga Wabwino, nakhulupire.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 15

Onani Macitidwe 15:7 nkhani