Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 14:26-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. komweko anacoka m'ngalawa kunka ku Antiokeya, kumene anaikizidwa ku cisomo ca Mulungu ku Ilchito imene adaimarizayo,

27. Pamene anafika nasonkhanitsa Mpingo anabwerezanso zomwe Mulungu anacita nao, kuti anatsegulira amitundu pa khomo la cikhulupiriro.

28. Ndipo anakhala pamenepo ndi akuphunzira nthawi yaikuru.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 14