Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 14:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

napfuula Dati, Anthuni, bwanji mucita zimenezi? ifenso tiri anthu a mkhalidwe wathu umodzimodzi ndi wanu, akulalikira kwa inu Uthenga Wabwino, wakuti musiye zinthu zacabe izi, nimutembenukire kwa Mulungu wamoyo, amene analenga zakumwamba ndi zapansi, ndi nyanja, ndi zonse ziri momwemo:

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 14

Onani Macitidwe 14:15 nkhani