Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 13:50-52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

50. Koma Ayuda anakakamiza akazi opembedza ndi omveka, ndi akulu a mudziwo, 12 nawautsira cizunzo Paulo ndi Bamaba, ndipo ana wapitikitsaiwom'malire ao.

51. Koma iwo, 13 m'mene adawasansirapfumbi la ku mapazi ao anadza ku Ikoniyo,

52. Ndipo 14 akuphunzira anadzazidwa ndi cimwemwe ndi Mzimu Woyera.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 13