Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 13:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Paulo ndi Bamaba analimbika mtima ponena, nati, 9 Kunafunika kuti mau a Mulungu ayambe alankhulidwe kwa inu. 10 Popeza muwakankha, nimudziyesera nokha osayenera moyo wosatha, taonani, titembenukira kwa amitundu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 13

Onani Macitidwe 13:46 nkhani