Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 13:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene atamcotsa iye, anawautsira Davine akhale mfumu yao; amenenso anamcitira umboni, nati, Ndapeza Davine, mwana wa Jese, munthu wa pamtima panga, amene adzacita cifuniro canga conse.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 13

Onani Macitidwe 13:22 nkhani