Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 12:22-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Ndipo anthu osonkhanidwawo anapfuula, Ndiwo mau a Mulungu, si a munthu ai.

23. Ndipo pomwepo mngelo wa Ambuye anamkantha, cifukwa sanampatsa Mulungu ulemerero; ndipo anadyedwa ndi mphutsi, natsirizika.

24. Koma mau a Mulungu anakula, nacurukitsa.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 12